Willz - Ndimaku Pempelela Lyrics

Lyrics Ndimaku Pempelela - Willz



Ndimaku
Kuku
Ndimaku
Kuku
Ndimakupempelako
Ndimakupempelako
Ndimakupempelako
Chauta anke wako
Kuti upesdza wako
Okonda mutima wako
Ndimakupempelako
Unga nkwale unayenda unanisiya
Ndimakupempelako
Mulungu eka ndiye aziwa
Ndimakupempelako
Sikulina ndiza pola
Ndimakupempelako
Hello Hello
Kodi unakwanisa
Kudzi peza zewenzo sakila Mu chikondi
Nikungo sifunsa ma funso
Kodi anaku pasa Zomeni ninalepa kuku pasa
Kodi ninalakwa chani Una kungo nisiya ko panda chifukwa
Natangwa nika
Nika kumbukila mau yako
Yochoka pakamwa kako
Unati sunga yende
Yankale Mabvuto yachuluke
Ndimakupempelako
Chauta anke wako
Kuti upesdza wako
Okonda mutima wako
Ndimakupempelako
Unga nkwale unayenda unanisiya
Ndimakupempelako
Mulungu eka ndiye aziwa
Ndimakupempelako
Sikulina ndiza pola
Ndimakupempelako
Iye Iye
Kodi umamudza umu konda
Kodi mutuma wako una kondwa
Kodi ukamu langa mumaso
Umanva chikondi
Chochoka pansi pamutima
Kodi suzamusiya naye
Kodi uzaka kalmba naye
Kodi ntawi zina mwe umaganizapo
Kuti wenane tinga bwezani
Kodi unga konde benaso
Mwina inga nkale Mphatso
Ayo ndima ganizo yanga
Anyway
Ndimakupempelako
Chauta anke wako
Kuti upesdza wako
Okonda mutima wako
Ndimakupempelako
Unga nkwale unayenda unanisiya
Ndimakupempelako
Mulungu eka ndiye aziwa
Ndimakupempelako
Sikulina ndiza pola
Ndimakupempelako
Ndimakupempelako
Chauta anke wako
Kuti upesdza wako
Okonda mutima wako
Ndimakupempelako
Unga nkwale unayenda unanisiya
Ndimakupempelako
Mulungu eka ndiye aziwa
Ndimakupempelako
Sikulina ndiza pola
Ndimakupempelako




Willz - Umoyo Wa Willy
Album Umoyo Wa Willy
date of release
21-09-2017




Attention! Feel free to leave feedback.