Zani Challe - Ndiphunzitse Lyrics

Lyrics Ndiphunzitse - Zani Challe



Anything you want for me to do, i do
Everything u want from me u know i do
Ndiphunzitse, ndiphunzitse eee
Zogwa nchikondi mama zikuopsa
Anzanga ambiri inu achimina
Akubwera mitima iliyosweka
Chikondi chokoma chija, chikusanduka inu chiphwinjo
Boy ngat wandikonda chonde ndiphunzitse ee
Chomwe umafuna chonde ndidziwitse ee
Chifukwa ulendo wachikondi, ndiwampaka mpaka
Zimafunika kusangalala aah
Yeeh eeh
Ndiphunzitse
Babe
Ndiphunzitse
Babe
Ndiphunzitse
Ndizikathyakula bwanji inee
Ndiphunzitse
Show me
Ndiphunzitse
Babe
Ndizikaoneka bwanji ine
Ndiphunzitse
Kaonekedwe
Ndiphunzitse
Chikhalidwe
Ndiphunzitse
Usakapeze wina
Ndiphunzitse
Ndiphunzitse ine
Ndiphunzitse
Ndionetse ine
Ndiphunzitse
Am ready, am ready, am ready show me
Zani challe
Uyayayo, uyakayaka yo
Ok
Ndakhonzeka kuvala mamini kamba ka weo
Am ready kubaisa mahip kamba ka wewo
Posaponda ine ndiponda, zokondawe ine ndikonda
Sindikufuna kukuluza
Zikumamvetsa chisoni, ma anja ambiri akutha, kamba kosagonjelana
Yeeea eeee
Ndiphunzitse
Babe
Ndiphunzitse
Babe
Ndiphunzitse
Ndiphunzitse ndizikathyakula bwanji ine
Ndiphunzitse
Show me
Ndiphunzitse
Babe
Ndizikaoneka bwanji ine
Ndiphunzitse
Kaonekedwe
Ndiphunzitse
Chikhalidwe
Ndiphunzitse
Usakapeze wina
Ndiphunzitse
Ndiphunzitse ine
Ndionetse ine, am ready, am ready, am ready show me
Trick on the beat (makina amwene)
Pro B on the board
Ummm mm
Malawian bway
Ummm mm
Uyayayo
Umm mm
Ok



Writer(s): zani michelle chiumia


Zani Challe - Ndiphunzitse
Album Ndiphunzitse
date of release
06-04-2016




Attention! Feel free to leave feedback.