James Sakala - Nilandileni - traduction des paroles en anglais

Paroles et traduction James Sakala - Nilandileni




Nilandileni
Nilandileni
Chikondi iyee ×5
My love, my love ×5
Nalila eyy nazo zapaziko
My darling, here I am with a good promise
Nadandaula ine nazo zapaziko ba zanga nee
I've come to you with a good promise, friend, my spouse
Ndaba uyu umoyo naupuzila molimba
I see that this life is full of hardships
N′nakana waulesi kana kulibikila
I can't advise or prepare
Koma lelo napeza chikondi chobambana eyy
But today I found a love that is matchless
Sichiziweza yai chilibe sanje aye
It's unchanging, it has no end
Chimapirira ichi nichikondi cha zoona
This covenant is a true love
Amalume nilandileni
My queen, tell me
Nabwela n'dchikondi chobambana chapaziko
I've come with a matchless love, a promise
Azanga nilandileni
My love, tell me
Nabwela n′dchikondi chobambana zapaziko zonse zintu(abale banga)
I've come with a matchless love, a promise of all things (my friends)
Ichi ni chikondi chochokela kwa abuye yesu.
This is a love that comes from our Savior Jesus.
(Ooh abale banga aayy)
(Oh, my friends)
Ichi nichikondi chochokela kwa abuye yesu
This is a love that comes from our Savior Jesus
Chikondi iyee×2
My love ×2
Nalema nazo zotukanidwa kwa bale banga aye
I've endured insults from my friends
Nalema nazo zonozidwa kwa alongozi banga
I've endured mockery from my leaders
Kodi sumumaona chisanzo chinasiya abuye yesu
Don't you see the example that our Savior Jesus left?
Sitigalese kubonya ma party wabo
We cannot keep attending their parties
Anadiya nao chimwa kubulumusa mbamba
With them, he eats and drinks to make the poor forget
Kuchilisa aliyense opanda usanka
To comfort everyone who has no joy
Uyu ndiye mutima nimafuna kukala nao ooh...
This is the heart I want to have
Mai kalanga neo
My dear lady
Amalumbe nilandileni
My queen, tell me
Nabwela n'dchikondi chobambana chapaziko
I've come with a matchless love, a promise
Azanga nilandileni
My love, tell me
Nabwela n'dchikondi chobambana zapaziko
I've come with a matchless love, a promise
Zonse zintu
Of all things
Ichi nichikondi chochokela kwa abuye yesu
This is a love that comes from our Savior Jesus
(Ichi nichikondi)
(This is a love)
Ichi nichikondi chochokela kwa abuye yesu×2
This is a love that comes from our Savior Jesus ×2
Chikondi ×3
Love ×3
Tiyeni tigilane manja
Let's join hands
Tiibenibo za chikondi×2
Let's be filled with love ×2
Oooh...
Oh...
Ichi chikondi chachokela kwa abuye yesu×2
This love that comes from our Savior Jesus ×2
Tiyeni tigilane manja
Let's join hands
Tiibenibo zachi nsaglalo...×2
Let's be filled with community ×2
Ichi chikondi chochokela kwa abuye yesu×2
This love that comes from our Savior Jesus ×2






Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.