Onesimus Muzik - Heavily Defended paroles de chanson

paroles de chanson Heavily Defended - Onesimus Muzik




Kwame Church: They don't see me well
Samakondwa name eeeeh
They don't want to be happy
Samagona nane tulo
Mulungu Wanga ndi wa moyo
Kulimbana nane simunditha
Nyanga zanu pa ineyo sizingamake (sizingamake)
Kwame Church: Maenje mwakumba mugwelamo Nokha
Misampha mwatchela mudzilasa nokha
Mukachita chibwana mudyedwa
Mukusewera ndi nkango (mukusewera ndi nkango)




Onesimus Muzik - EPIKAIZO vol.2
Album EPIKAIZO vol.2
date de sortie
11-01-2016





Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.