paroles de chanson Lay Low - Phyzix feat. Krazie G & BFB
It's
only
entertainment,
exclusive
(Hook)
Timangomenya
ma
beat,
timadziwika
Mzuzu
B-Town
and
L-CITY
Yeah
Timangomenya
ma
heat,
tikakwela
pa
stage
timasiya
mbilri
Awo
amatihater
awo
awo,
koma
imatifila
chick
yawo
Amatihater
awo
awo,
hey
I
let
go
call
me
lay
low
(Phyzix)
Ine
ndi
Gamba
wa
suit,
I
am
from
25
and
I
rep
L-CITY
Tinasintha
ma
levels,
straight
outta
the
ghetto
uzandipeza
pa
office
Kufilika
kwa
ineyo
sikwa
season,
Chaka
chilichose
ndimatulusa
ma
ringtone
Competition
ya
ineyo
ndi
nsima
timapikisana
kupezeka
nyumba
zonse
Competition
ina
ndi
instrumental,
timapikisana
kupezeka
nyimbo
zonse
Amanditcha
Phyzo
mfana
wotha
zinthuzi,
Ma
baby
akungonditenga
zithunzi
Ma
selfie
ma
selfie
ndi
selfie
stick
Si
ine
short
ngati
Dizzo,
ndine
captain
long
John
Mfana
womveledwa
ngati
mastern
Mfana
wazigoli
ngati
Messi
10
(Hook)
(Kraizy
G)
King
katakwe
eyy
yoh
eyy
you
(yes
sir)
Odi...
Mfumu
katakwe
ilipo?
Ilipo
iwe
ukufunsa
ngati
ndaniso?
Kodi...
Anthu
akewa
sagwilila
ntchito?
Ntchito?
Kwaiye
ntchito
ilibe
ntchito...
(huh)
Basi
chete
mfumu
itiyankhule
Timafana
todelelati
nditibandule
Chaka
Chino
ma
guy
akupaka
nditchule
Ndipo
ma
guys
azingovina
aise
azingovina
Mfana
ati
Ali
sick,
akangomenya
three
bars
bas
Akuti...
Amupeza
ndi
ma
asthma
Ndikuti
ndikudwala
zi
marasmus
Looks
ya
hd
mboni
ndizimaplasmas
Ada...
ndinafika
nazo
pauchitsiru
Moti
mafana
panopa,
amangodibela
skill
Uchitsiru
aise...
Ndili
ndi
skill
Ndinapha
hip-hop,
ndikupezekaso
pa
will
(Hook)
(Black
falcon
Bird
-BFB)
Ife
ndi
nkhaza...
We
kill
beats
and
the
flows
no
limit
Mafana
akunama,
R.I.P
to
Mafunyeta
no
gimmick
It's
just
me
and
everybody
supporting
the
movement
Heard'em
you
rappers
we're
going
we're
moving
Tell'em
these
we're
winning
no
loosing
Remember
I
am
smart,
I
am
the
one
God
has
chosen
Kuwakupa
mafana,
mpakana
akunena
tchuzi
Sinanga
ndine
mfana
wotenthetsa
ngati
juzi
Sinanga
Iwo
sioyimba,
ine
mtengo
Iwo
mthunzi
Kuphatikiza
Ngwazi,
Dr.
Bingu
ndi
Muluzi
I've
brought
a
new
style
called
payele
payele
Umayesa
umatha,
kagwele
kagwele
And
the
verse
that
I
have,
dzamvele
dzamvele
Mfana
wadzimbidwa
aka...
haaa
haaaa!!!
(Hook)
The
End
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.