Emrys Amaré - Ndiwe Okongola Lyrics

Lyrics Ndiwe Okongola - Emrys Amaré



M'mene umayendela
Namwali wamanyazi
Ukuyang'ana pansi
Poti suudziwa suudziwa
Ukamandisekelela
Mtima wanga mthumadzi
Iwe ndiwe nyenyezi
Koma suudziwa suudziwa
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Dzuwa linabisala
M'lungu analenga iwe
Mwenzi unanyanyala
Pokuwona iwe ukuwala
Ine ndimasangala
Iwe ndiwe nthiti yanga
Ndithu ndiwe mtetezi
Wa mtima wanga
Mtimanga
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!
Ndiwe okongola!



Writer(s): Emrys Amaré


Emrys Amaré - Lilting Rhymes of Lilac
Album Lilting Rhymes of Lilac
date of release
30-04-2019



Attention! Feel free to leave feedback.