Gwamba - Unatha текст песни

Текст песни Unatha - Gwamba



Intro (Gwamba)
Ase Gwamba(mmmh) uli kutiko?
(Ndikuvaya ku church aise)
Iyayi, panopa tacaller Zima chick aise,
Kuli zi ma chick 6 zinazake (Iyayi man
Ndikuvaya ku church ase) 4 za ku CU, 2 za ku DMI
(Iii ase Lero nde Friday nde timavaya ku church)
Tagula mikunda, shisha, inunso amwene
(Simungazimvetse)
Yo
Unali kale aise uli ndi ma chick ten
Amachita kukumana kupasana ma turn
Lero kubwela Mary mawa kubwela Jane
Pakamwa pako Nthawi zonse Mary Jane
Pano kukucaller Friday uli ku church
Team yamadolo mphwanga uli pa bench
Iwe kumapemphela ife tikuwupeza
Man Gwamba anakupusitsani Major
Timamenya drug, Timamenya bagi
Maluzi kubwela iwe kupinyulitsa Shati
Nthawi Zina akabwela kupinyulitsa car key
Umakonda mabomba timakutcha Iraq
UNALI KALE IWEEE
Pano suzitsata, tikamenya beef nanga bwanji sutiyankha
UNALI KALE IWEEE
Pano suli ghatta, ukuimba zotukwana muja unkatiwaza
×2
Nde Man Gwamba simubwela?
EHHHHH AISEE DAMAN (Shut up in Hebrew)
Zomwe mupangazo ndinapanga kukuposani
Ndikudziwa bwino moyo musapange makani
Kuzitchela nokha mawali muli pampani
Man, zimenezo mumapindula chani?
Kuononga dola, kufuna kuballer,
Mawa kufuna kugula phax nthumba osalola
Mwadzuka ndi Flora, komano ndi mbola
Chifukwa aliyense Ali ndi dola amamucaller
Komani man, ndinu friend osamakhala chonchi
Mumuyese Yesu Khristu otifela pa cross
Mukapeza Nthawi mutipezeko ku temple
Mawu aNamalenga aja muzawamveko
UKALE KALE IWE
UNALI KALE IWE
GWAMBA UNALI KALE IWE
UNATHA
(AK)
Ayayayayayaya
Ayeeeeye
Ayayayayayaya
Ayeye
Ayayayayayaya
Ayeye
Ayayayayayaya
Ayeye
You can download the song below



Авторы: A.k., Bfb, Fredokiss, Tiya


Gwamba - Unatha
Альбом Unatha
дата релиза
22-07-2019

1 Unatha




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.