Eli Njuchi - Why Songtexte

Songtexte Why - Eli Njuchi




Yeah, yeah, yeah
J-Mas
J-Mas
Njuchi
(Savage)
Ay, ay
(On the beat)
Yeah, yeah
Dear ma hope
Ndalimba mtima lero Sangie
Sindikudziwa zitha bwanji?
Sumandiyankha pa Facebook, Insta, Twitter Nanji
Ma bluetick onswewa bwanji?
I've been following you mayi wa ngwiro
Kuyambira form one mpaka four
Every show ndimakhala Konko, sindinajombeko
Sangie, ukundithela bundle
Kapena mwina chifukwa ndine mwana? Sangie
Sizikugwirizana, Sangie
Mesa tidzikondana
Ndiyankhe njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tikakumana kwa Sispence
All I get ndi aire basi
Sangafile Njuchi alibe VW
Akatha mtunda ndi minibus
Ndikati ndipemphe selfie uli busy
Ndikhole number ili busy
Ayi busy
Still I do it all for love
Ndiyankhe Njuchi aku-, uh
Kapena mwina chifukwa ndine mwana? Sangie
Sizikugwirizana, Sangie
Mesa tidzikondana
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire
Tell me why?
Tell me why?
Tell me why?
Ndiyankhe Njuchi akukakamire



Autor(en): Eli Njuchi


Eli Njuchi - Why
Album Why
Veröffentlichungsdatum
18-12-2021

1 Why




Attention! Feel free to leave feedback.