Achina Gattah Ase - Street Lyrics

Lyrics Street - Achina Gattah Ase



Achina Gattah Ase
Kutchuka kochoka ndix mpaka manase
Yoo...
Ngat rapper wako anaimba ndine anafa
Ngat rapper wako sanaimbe ndne samatha
Ndye kwa mafana nonse ofuna kuimba ndine simumanva
Osadanda ndkubwela posachedwa "maranatha"
Ndikuzapha mafana a sh*t
(Sindikupola)
Ili nd bala la mfana wa sick
Ndinasowa, Quarantine ndi mafana a sick
Ati ma Elder... ndine?
(F*ck that sh*t)
Ine nd king wa streets
Ndapulumus game at least
Checker nomination list
Am like going on . please
Gattah new comer
Mwin chifukw cha high demand
Judge anakanika ku judger anangowapasa mafana remand
Nanga anakapanga bwanj naye amaopa ku brander
Ndinalowa 100 kugula cheese
Crew yanga yonse kubanda
Guardian wa new xool mafana mumakumva ku hander
Azifumu mbama . ine nd
Gwanda chakwamba
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd mmmmmm!!!
Ndapulumusa game at least
Checker nomination list
Am like going on. please
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd king wa streets
Ine nd king wa gist
Ine nd mmmmmm!!
Ndapulumusa game at least
Checker pa ma artist list
Pan Rest In Peace
Yoo.
Game pakatip inagona
Musayese ngat mafumu sitimaon
Ma rapper omwe ndnadiwis kunkhondo zomvesa chisoni onse anathel konko
Of course sanadiwe km
Anashal moshko
Anasiya chamba cha hiphop
Anayamba chakonko
Kuyamba kuimba pakanthawi
Akuzimva alimomo
Munthu sumakhal legend
Chifukwa ndwe Gogo
Mafana amvula zakale si size yanga ndawavulaza kale
Kuwaveka khofi kuwavula zakal
Ndinangowawelenga nkuwachit
Summary
I took the game back to BT'z
I don't give a f*ck
But your not my real geez
Kugwila rapper nkhwiko
Mpaka ngozi
Chifukw ndli Inkosi ya Makosi
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd mmmmmm!!!
Ndapulumusa game at least
Checker nomination list
Am like going on. please
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd king wa streets
Ine nd mfumu ya gist
Ine nd mmmmmm!!
Checker pa ma artist list
Pan Rest In Peace
Yoo.
Ma rapper mu game mwangozazana
Zi beef mukungodya km nzazan
Umanva bwanj Gattah akat "ndwe new comer".?
Kutenga Spliff kumenya pur
Nkudya hahahaha...
EC22



Writer(s): Mike Desmond Mkhaya


Achina Gattah Ase - Street
Album Street
date of release
29-03-2021

1 Street




Attention! Feel free to leave feedback.