Lyrics Ndiwe Okongola - Emrys Amaré
M'mene
umayendela
Namwali
wamanyazi
Ukuyang'ana
pansi
Poti
suudziwa
suudziwa
Ukamandisekelela
Mtima
wanga
mthumadzi
Iwe
ndiwe
nyenyezi
Koma
suudziwa
suudziwa
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Dzuwa
linabisala
M'lungu
analenga
iwe
Mwenzi
unanyanyala
Pokuwona
iwe
ukuwala
Ine
ndimasangala
Iwe
ndiwe
nthiti
yanga
Ndithu
ndiwe
mtetezi
Wa
mtima
wanga
Mtimanga
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Ndiwe
okongola!
Attention! Feel free to leave feedback.