Naomi - Ambuye Wanga Lyrics

Lyrics Ambuye Wanga - Naomi




Ambuye wanga, mbuye wanga, mbuye wanga,
Ndagwa pamapazi yanu ine munthu wamachimo ine, mbuye wanga 2x
Wazizimuka mtima wanga mbuye mulungu wachifundo ine mbuye wanga
Ndazizwa pama chimo yanga simumanditailila mbuye wanga ine
Muchifundo chanu
Mbuye mulungu chifundo chanu ndichachikulu ndavomera ine mwana wanu
Ndikachimwa simumandilanga
Mumandipasa nthawi yolapa ine machimo yanga...
Lizzilitious.com




Naomi - Nadza Kwa Inu
Album Nadza Kwa Inu
date of release
20-09-2015




Attention! Feel free to leave feedback.