Phyzix feat. Dette Flow, Crispy Mw & Nitrix - Zibwente Lyrics

Lyrics Zibwente - Phyzix feat. Dette Flow, Crispy Mw & Nitrix



Captain bae
Kwa ma hope anga amagulisa zibwente
Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10
Ndikafuna ku chiller
Ndimatenga dollar ya zibwente
Ndi chilichonxe cha Ben 10
Ndikatelo am in
Skueeww
Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4
Yoooh
Amaoneka sizimamukhuza
Zoti ndine mfana otchuka
Amaoneka sizimamisutha
Olo number yake amakaniza ...
Koma zibwente zokhazo nde ndimagula
Kuti mwina nthawi yochiller naye izichuluka
Ndine captain bae
Bae wako ndi bae chabe
Ndine captain bae
Bae wako ndi bae chabe
Kwa ma hope anga amagulisa zibwente
Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10
Ndikafuna ku chiller
Ndimatenga dollar ya zibwente
Ndi chilichonxe cha Ben 10
Ndikatelo am in
Skueeww
Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4
Ndigotenga hanz
Ndikagonama ngat ndikufuna zibwente
Kenako ndipange chimasamu kuti man
Ka Chick nditenge
Ine ndi mfana wa chabe
Kasitomala wa masten ake
Best friend wa broz yake
Ndimagolowa ndiya zibwente
Amake a Lisa
Ndikufuna zibwente
Ngat chenje chikuvuta Masten
Mumuuze Lisa atenge
Kwa ma hope anga amagulisa zibwente
Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10
Ndikafuna ku chiller
Ndimatenga dollar ya zibwente
Ndi chilichonxe cha Ben 10
Ndikatelo am in
Skueeww
Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4
Malawi
Kudya zibwente za ten
Za twenty
Thirty
Za fifty
Ndi watch yokha ya Ben 10
Broz yake singalimbe
She was like clispy u feel this
Coz u crazy G
Nanga zigenge za twenty
Za thirty zomwez
Mpaka kumwela tea
Ndamuthoka kuti
Ndine captain bae
Bae wako ndi bae chabe
Ndine captain bae
Bae wako ndi bae chabe
Kwa ma hope anga amagulisa zibwente
Broz yake imakonda ma cartoon a ben 10
Ndikafuna ku chiller
Ndimatenga dollar ya zibwente
Ndi chilichonxe cha Ben 10
Ndikatelo am in
Skueeww
Kudya kudya kudya kundya kudya Zibwente(Turn up)×4



Writer(s): Asodzi, Bfb, Phyzix


Phyzix feat. Dette Flow, Crispy Mw & Nitrix - Zibwente
Album Zibwente
date of release
13-09-2017



Attention! Feel free to leave feedback.