Rudimental feat. The Martinez Brothers & Faith Mussa - Sitigawana (feat. Faith Mussa) Lyrics

Lyrics Sitigawana (feat. Faith Mussa) - Rudimental feat. The Martinez Brothers & Faith Mussa



A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh
A Phiri anabwela kuchoka ku Harare eeh
Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza "
Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara"
A Phiri anaganiza "
Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse
Anamwalira ku Dara
••• Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza "
Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse Anamwalira ku Dara"
Anamwalira ku Dara
Oh sitigawana!
•••
Oh sitigawana!
Sitigawana
Oh sitigawana zida
Umandikondera M'mene umandikondera Ife
Sitigawana zida
Sitigawana
Sitigawana zida
Sitigawana
Ife sitigawana Sitigawana
Oh sitigawana zida
Sitigawana!
Sitigawana!
Oh sitigawana zida
Umandikondera
M'mene umandikondera
Ife sitigawana zida
Sitigawana!
Sitigawana!
Oh sitigawana zida
Umandikondera M'mene umandikondera
Anamwalira ku Dara
•••
Koma nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
Ndati nkati mwa suitcase Munalibe kanthu shuwa
A Phiri anaganiza "
Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse Anamwalira ku Dara" A Phiri anaganiza "
Kodi ndidzayenda kuti?
Makolo anga onse Anamwalira ku Dara" •••



Writer(s): Christian Martinez, Amir Izadkhah, Piers Aggett, Kesi Dryden, Leon Rolle, Steve Martinez Jr, Faith Mussa, Nashil Pichen Kazembe


Rudimental feat. The Martinez Brothers & Faith Mussa - Sitigawana (feat. Faith Mussa)
Album Sitigawana (feat. Faith Mussa)
date of release
21-06-2019




Attention! Feel free to leave feedback.