paroles de chanson Ndamusowa - Armstrong
Kupita
masiku
angapo,
Osamuona
kukhala
ngati
zaka
No
texting,
no
hello
saying
darli
Sizikuenda
Usiku
onse
osagona
Masana
kumaganiza
iwe
dona
Kalalaka
mtakuona
Usiku
onse
osagona
masana
kumaganiza
iwe
donaa
Sindichitiraso
mwina
ine
Ndipita
kwawo,
kwawo
konko
Mkamuuze
ndimakukonda
Ndipita
kwawo
kwawo
konko
Mkamuuze
ndamusowa
Oh
na
na
na
ndamusowa
Oh
na
na
na
ndamusowa
Oh
na
na
na
ndimamukonda
Oh
na
na
na
ndimamukonda
Oh
na
na
na
ndamusowa
Oh
na
na
na!
ndamusowa
Mtima
wanga
umawa
Ukatalikira
ndimadwala
Achina
fever,
ma
injections
Can
never
heal
me
Oh
baiby,
ndimasowa
mtendere
Eeeh
eeh
hee
Usiku
onse
osagona
Masana
kumaganiza
iwe
dona
Kalalaka
mtakuona
Usiku
onse
osagona
masana
kumaganiza
iwe
donaa
Sindichitiraso
mwina
ine
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.