BigPhil - Banja Limatha paroles de chanson

paroles de chanson Banja Limatha - BigPhil

Ab-Dul with the sauce
N'dalitu ndi matha ine n'dali ndi mantha
Chikondi tida manga iwe Ku manga pa mwala
Kuwopa ku vulala ine n'dali ndi mantha
Mayina tidasankha iwe dzina la mwana
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha

We were so in love
So young So Blind
We were making plans
My wife for life
The way you held me tight
That night it felt right
Now we fell apart
Ain't no way to rewind
It was love phwamwamwa
Koma phuma osamva
Ife tinagwa chagada
Koma love Sakaka
Baby girl tidanyanya
Kuli konse undi tsata
Koma love Ida Mata
Olo banja litatha
N'dalitu ndi matha ine n'dali ndi mantha
Chikondi tida manga iwe Ku manga pa mwala
Kuwopa ku vulala ine n'dali ndi mantha
Mayina tidasankha iwe dzina la mwana
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha
N'dalitu ndi matha ine n'dali ndi mantha
Chikondi tida manga iwe Ku manga pa mwala
Ndati banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha
Banja limatha iwe Koma Chikondi nchosatha

Writer(s): Nthangwanika Kondowe

BigPhil - Phases
Album Phases
date de sortie
13-11-2021

Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.