Gwamba - Kusasa Mawu paroles de chanson

paroles de chanson Kusasa Mawu - Gwamba



Ndiyimbila yehovah ine .
Mpaka kusasa mawu ine wandipatsa ka girl timaso tamngero...
Ndiyimbila yehovah yoh mpaka kusasa mawu ine
Wandipatsa ka girl timaso tamngero relo ndisasa mawu...
Yeah ambuye mwadyetsa mbalame zosalima.
Kundionetsa njira nditangoima.
Kufewetsa moyo wanga ukulimba.
Mwandipatsa mkazi mkona ndikuyimba.
Nditangomuona thupi langa lose kugwidwa zazi.




Gwamba - Kusasa Mawu
Album Kusasa Mawu
date de sortie
27-07-2018




Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.