Gwamba - Mbama paroles de chanson

paroles de chanson Mbama - Gwamba



Malawi music.com
Nyimbo zachimalawi
Aaah aah
Sley
DJ sley
Yaaah
Kumuvetsa kuwawa jabu
Mbama, theche, sitoz
Alipasi
Ndamuuza satana pita kutali usandilonde mapazi
Kung fu, judo,
Eehshi
Ali mdothi
Ndamuuza satana pita kutali osandipanga approach
Mbama, theche, stozi
Alipasi
Ndamuuza satana pita kutali usandilonde mapazi
Kung fu, judo,
Eehshi
Ali mdothi
Ndamuuza Satana pita kutali osandipanga approach
Ali ndi anthu ake
Ali ndi anthu ake jabu
Ukaona kuwala amabwera kuzimitsa bulb
Ali ndi anthu anthu ake rusifala
Ukamakwera mwamba amakukoka musidala
Njala, thenda
Amabweretsa ndi devil
Popanda mau amulungu ndukuuza pawekha sungalimbepo
Khala, dekha
Nkhondoyi ndiyauzimu
Amamenya nkhondo mulungu yekha ziwanda zili ka team
Nde or mavuto kubwera ndimangotenga Bible langa
Ndikawelenga kokwana
Ndimangodzifila ngati chi phaza
Devil kutuma ziwanda(eti)
Devil kutuma ziwanda(eti)
Koma ndimaziuza pita kwamene
Wakutumayo




Gwamba - In Advance
Album In Advance
date de sortie
19-02-2018




Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.