Khetwayo - Disenimenti paroles de chanson

paroles de chanson Disenimenti - Khetwayo



Mau a Mulungu kuchita kuchekenera
Kutsira nsinjiro kuchita kutendelera
Nkhosa za Mulungu kuchita kuwendelera
Kukakamiza moto kuchita kupemelera
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Trana shoot my shot and chill while my net flix
With shorty to build with like tetris
My pride let go couple of relics
I never knew better on discernment
Am at a point where
I got a lot of questions
A dog-collar don't mean I know better
Am at a point where
I check my intentions
She looks fine but my God look better
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Mau a Mulungu kuchita kuchekenera
Kutsira nsinjiro kuchita kutendelera
Nkhosa za Mulungu kuchita kuwendelera
Kukakamiza moto kuchita kupemelera
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Akangodumpha aliyense akudumpha
Akangosuntha aliyense akusuntha
M'manja pamoto kufuna kuphula
Aint nobody asking why akudya phula
I stand corrected
Never mistake the facts from hatred
My generation wanna be emancipated
From religion which is highly
Weighted fabricated
Now see their gains are fading
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Mau a Mulungu kuchita kuchekenera
Kutsira nsinjiro kuchita kutendelera
Nkhosa za Mulungu kuchita kuwendelera
Kukakamiza moto kuchita kupemelera
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Apapa palufunika disenimenti
Palufunika disenimenti
Inu disenimenti
Diseniment diseniment
Disenimenti
Inu disenimenti
Diseniment diseniment
Disenimenti
Apa Palufunika disenimenti
Palufunika diseniment
Apa Palufunika disenimenti
Palufunika diseniment
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Mundithandize nchidziwitso
Kwachuluka kudyetsana phula
M'matipatsa aulere madalitso
Pamene ena achita kugula ah
Inu disenimenti
Diseniment diseniment
Disenimenti
Inu disenimenti
Diseniment diseniment
Disenimenti
Apa Palufunika disenimenti
Palufunika diseniment
Apa Palufunika disenimenti
Palufunika diseniment




Khetwayo - Worth Waiting For
Album Worth Waiting For
date de sortie
30-09-2022




Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.