Slap Dee - Dzuwa (feat. Jorzi) paroles de chanson

paroles de chanson Dzuwa (feat. Jorzi) - Slap Dee



Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko langenewa nguwe
Tasudzika kopanda dzuwa
Ooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga yangenewa tululu
Tiyamika mweo apo pa mupando
Dzuwa dzuwa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko langewa nguwe
Tasudzika kopanda dzuwa
Ooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga yangenewa tululu
Tiyamika mweo apo pa mupando
Dzuwa dzuwa dzuwa
Nakana ku believer ndise tili naminyama
Navemzo nvekamunshe vinaleka nakuwama
Tinalakwila ndani mutikambileko sorry
Mayeso yatikonka bad izibika story
First yenze cholera kwabwela loadshading
Before nama corona tenze busy nama gassing
Tayamba opayana tekataka it's so disgusting
Namabusa balema navo vama fasting
Ku hood kwanga ba guy bafunache ka certain
Bavale che pamala na ka nsima ndiye curtain
Sibafuna nanvambili umoyo che ni Dalitso
Ambuye abwezepo nga muchila wamalinso
How did we get here nalema kuzinfunsa
Kapena niudalu sinasize pa unza
Agogo ananiuza azakula mwana chipuba
Vikakuvuta langa kumwamba upempe dzuba
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko langenewa nguwe
Tasudzika kopanda dzuwa
Ooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga yangenewa tululu
Tiyamika mweo apo pa mupando
Dzuwa dzuwa
Dzuwa
Nauka muthu uzunguka monga nenze pakampelwa
PA fb tayali akalu menyana na mwewa
Could it be that am stressing am Making a big fas
I know that there is somebody looking for a face mask
Cause they die without a proper doctor and a nurse
Without the medication they'll end up in a harse
Are we born with a gift or maybe blessed with a curse
With the afterlife uncertain we might end up in a church.
Just Not long ago nenzonvelela seer 1
Enze once a topic patu Napa bondi panu
Since when chinfine chanankalapo big issue?
Sambani kumanja sanitize nama tissue
Now all my shows canceled am living off my investments
Pray to God he saves my family and my best friends
Everything Quarantined house, money, car
Pray for Zambia, for the globe, for Africa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko langenewa nguwe
Tasudzika kopanda dzuwa
Ooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga yangenewa tululu
Tiyamika mweo apo pa mupando
Dzuwa dzuwa
Dzuwa
Ambuye chosani dzuwa
Dziko langewa nguwe
Tasudzika kopanda dzuwa
Ooh dzuwa
Ambuye tidaliseni ndi dzuwa
Dziko lichita nga yangenewa tululu
Tiyamika mweo apo pa mupando
Dzuwa dzuwa dzuwa



Writer(s): Slap Dee


Slap Dee - Dzuwa
Album Dzuwa
date de sortie
01-04-2020




Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.