paroles de chanson Hear Me - The Very Best
CHICHEWA
Siyani
dumbo
Siyani
umbombo
Tatopa
nazo
kodi
simukudziwa
kuti
lija
ndi
kale?
Siya
umbanda
Siya
zauchigawenga
Kodi
watani
iwe
siukudziwa
kuti
kupha
ndi
sambi?
Siyani
dumbo
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Siya
kaduka
Siya
zokonda
kuba
Siyani
chinyengo
kuyambila
lero
tiyeni
tikonze
tsogolo
Siyani
kugona
Siya
kugona
tulo
Kunja
kwacha
kodi
simukuona
kuti
dzuwa
latuluka?
Siya
kaduka
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Hear
me
now
Dzaka
makumi
asanu
Zatha
kufika
lero
Mpaka
lero
umphawi
Ukungophabe
dziko
Dzaka
makumi
asanu
Zatha
kufika
lero
Mpaka
lero
umphawi
Ukungophabe
dziko
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.