paroles de chanson Ndabalalika - Zeze Kingston feat. XDuppy & Vj Ice
Mwana
wanga
Ngati
umandikonda,
mvetsela
Mwana
wanga
Ngati
umaukonda
moyo
wako
sintha
Mwana
wanga
Ngati
umandikonda,
mvetsela
Mwana
wanga
Ngati
umaukonda
moyo
wako
sintha
Ndati
palibe,
palibe,
palibe
Angakugwile
dzanja,
pamavuto
Ndati
palibe,
palibe,
palibe
Angakugwile
dzanja,
pamavuto
mwanawe
Uuuuh
Mwana
wanga
mvetsela,
mvetsela
Uuuuh
Mwana
wanga
mvetsela,
mvetsela
Komabe
njoya,
mosamala
poti
nkhondo
ndi
anansi
Amabwela
ngati
achibale,
koma
mpeni
atapanila
kuphanzi
Komabe
njoya,
mosamala
poti
nkhondo
ndi
anansi,
Amabwela
ngati
achibale,
koma
mpeni
atapanila
kuphanzi
Uuuuh
Mwana
wanga
mvetsela,
Mvetsela
Uuuuh
Mwana
wanga
mvetsela,
mvetsela
Komabe
njoya,
mosamala
poti
nkhondo
ndi
anansi
Amabwela
ngati
achibale,
koma
mpeni
atapanila
kuphanzi
Komabe
njoya,
mosamala
poti
nkhondo
ndi
anansi,
Amabwela
ngati
achibale,
koma
mpeni
atapanila
kuphanzi
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.