Текст песни KUKOPELA. - remix - Charisma Madness feat. Lolli Native, Bee Jay, Malinga & Chizmo Sting
Ku
ding
dong
aliko
Ku
ghetto
alikoso
Ku
ntchito
aliko
ma
copy
cut
ayi
nono
This
is
the
remix
we
don't
take
it
easy
This
is
the
remix
Madness
we
the
baddest
baddest
let's
go
Ukayamba
geni
ma
guy
akubwela
ati
nafeso
Moyo
okopela
pamalawi
wanyanya
tisanamepo
Ndikavalabo
kutchena
afuna
avaleko
Chinawatsalila
mchiwanda
chowonela
mayeso
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Look
what
I
did
for
my
People
in
Transkei
Thati
Xhosa
Rap
from
Capetown
to
Blantyre
Ndisphana
ndzima
Tryna
Raise
Flag
High
Kodwa
BombaKlyde
wanna
move
like
I
did
Tryna
Walk
in
these
shoes
and
its
my
Feet
Ingxaki
yam
I
yam
I
wanted
all
of
us
to
Win
Ungandbuzi
ndenze
Njani
God
Did
Ngenxa
yomona
yo'll
tried
kill
my
Dream
Why
u
hate
I
n
I
Numi
ngiPhume
kasi
I
thought
you'd
wanna
see
me
Shine
Sgaphikisani
this
is
my
time
Bhudda
of
the
Year
made
Xhosa
Rap
Fly!
Ndithi
Abanye
Bayakhopelaaa
And
Bona
Fostelaaa
NdiyaKhumbula
BesBomonela
Basbona
swinaa
bayaSondela
Mpaka
Akukopela
kotenga
ngongole
Kodi
mwakongolako
Tipeza
munthu
Mm
achimwene
Nafe
Tizitapee
Ntchito
ya
mutu
ndikudyelapo
Masuku
Paja
Ndadabwa
Adhawa
Kwatsalaku
Cash
adzaipanga
Photocopy
Mm
Sinanga
Sagwila
money
Ife
timaigwila
Ngati
0-40
Ndikahopela
nkazi
Nawo
Akuhopela
Ndikalowelela
Nawoso
Akusochela
Ukati
ukhwefule
nawo
akukhwefula
Usakhwefule
nawo
Troggi
akukokela
Chabwino
ndingoyamba
Geni
ndipange
ndalama
koma
Ukayamba
geni
ma
guy
akubwela
ati
nafeso
Moyo
okopela
pamalawi
wanyanya
tisanamepo
Ndikavalabo
kutchena
afuna
avaleko
Chinawatsalila
mchiwanda
chowonela
mayeso
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Akubela
man
Davie
afuna
awafile
Madonna
Chilichonse
photocopy
I
think
waachulukila
tonner
Anzao
akuphanda
iwo
akubanda
ku
mpanda
Akuti
ma
stonner
Nzao
uja
wasiya
geli
nawonso
asiya
nao,
koma
boys
sizoona
A
kujaiva
ngini
yoti
siyawo
Anadaiva
ref
caller
foul
Akuliva
ghetto
kubela
ding
dong
Lero
ndiize
awathamangitsa
kwao
Control
C
Control
V
Funa
kubela
Genna
from
18B
Don't
play
with
yo
future
anzanu
mukubela
wo
Makolo
awo
ali
ndi
plan
B
Di
world
ah
full
ah
bad
people
Dem
no
like
fi
see
di
Ras
ah
drive
vehicle
Ah
nuff
ah
Dem
ah
evil
No
wan
see
mi
rise
to
ah
higher
level
Ah
dem
just
can't
let
me
Bee
nao
afuna
akhale
Njuchi
Zonse
zabwino
akhale
Ndiwo
Ali
Msuzi
Ndikangodya
pause
nao
anvekere
tchuzi
Angotengera
zilizonse
mpaka
atenga
Edzi
Sting
dem
hard
man
ah
copier
fire
burn
Sungandiwalire
u
can't
copy
di
sun
Kunvetsa
chison
musamachite
makan
Popanda
likasa
ndinu
ma
zero
pa
ten
Ah
we
burn
di
fire
Iwo
amangopala
Ah
we
burn
di
fire
Iwo
amangopala
Ukayamba
geni
ma
guy
akubwela
ati
nafeso
Moyo
okopela
pamalawi
wanyanya
tisanamepo
Ndikavalabo
kutchena
afuna
avaleko
Chinawatsalila
mchiwanda
chowonela
mayeso
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Kopela
chilichose
kopela
Akangoonela
chilichose
kopela
Альбом
KUKOPELA. (feat. Lolli Native, Bee Jay, Malinga & Chizmo Sting) [remix] - Single
дата релиза
22-11-2022
Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.