Eli Njuchi - Gold Digger текст песни

Текст песни Gold Digger - Eli Njuchi



Sooner tinamvana zochita
Sindinachedwe kugwetsa number
Osadziwa unali mamba
Tima night calls titayamba
Tinka textana ku DM
Simene zinkabhebhela
Osadziwa unali mamba
Chikondi changa chasanduka ntanji
Kufasa kwanga mwapezako mwayi
Nyamukani kwanu mukanene
Kapezeni mgodi wina mukakumbe
Chikondi changa chasanduka ntanji
Kufatsa kwanga mwapezako mwayi
Nyamukani kwanu mukanene
Kapezeni mgodi wina mukakumbe
Ndiwe gold digger
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
I fell in love with a gold digger
Ndiwe gold digger iwe
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
A fell in love with a gold digger (gold digger)
Unasitha Zochita
Utamaliza kutenga zonse
You broke my heart into pieces
Eya gold digger
I hope you got what you wanted
Was it my body or my diamonds
I gave you my time and my feelings
Ndi moyo wanga that i invested
Zikumandiwawa i wasted my energy on you
Ndadana ndazizanga for defending you
Sine otchipa
Muthune ndine odula
It's only that you can't afford me
Ndika fake life kapa Insta
Siine Otchipa
Munthune ndine odula
Bambo ndinu gold digger
Ndika fake life kapa Twitter
Chikondi changa chasanduka ntanji
Kufasa kwanga mwapezako mwayi
Nyamukani kwanu mukanene
Kapezeni mgodi wina mukakumbe
Chikondi changa chasanduka ntanji
Kufatsa kwanga mwapezako mwayi
Nyamukani kwanu mukanene
Kapezeni mgodi wina mukakumbe
Ndiwe gold digger
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
A fell in love with a gold digger(gold digger)
Ndiwe Gold Digger Iwe
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
I fell in love with a gold digger
Ndiwe gold digger
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
A fell in love with a gold digger(gold digger)
Ndiwe gold digger
Mtima wanga sungakane
Ngakhale anzanga sangakane
A fell in love with a gold digger(gold digger)




Eli Njuchi - Red Flag
Альбом Red Flag
дата релиза
31-07-2022




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.