Текст песни Why - Eli Njuchi
Yeah,
yeah,
yeah
J-Mas
J-Mas
Njuchi
(Savage)
Ay,
ay
(On
the
beat)
Yeah,
yeah
Dear
ma
hope
Ndalimba
mtima
lero
Sangie
Sindikudziwa
zitha
bwanji?
Sumandiyankha
pa
Facebook,
Insta,
Twitter
Nanji
Ma
bluetick
onswewa
bwanji?
I've
been
following
you
mayi
wa
ngwiro
Kuyambira
form
one
mpaka
four
Every
show
ndimakhala
Konko,
sindinajombeko
Sangie,
ukundithela
bundle
Kapena
mwina
chifukwa
ndine
mwana?
Sangie
Sizikugwirizana,
Sangie
Mesa
tidzikondana
Ndiyankhe
njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tikakumana
kwa
Sispence
All
I
get
ndi
aire
basi
Sangafile
Njuchi
alibe
VW
Akatha
mtunda
ndi
minibus
Ndikati
ndipemphe
selfie
uli
busy
Ndikhole
number
ili
busy
Ayi
busy
Still
I
do
it
all
for
love
Ndiyankhe
Njuchi
aku-,
uh
Kapena
mwina
chifukwa
ndine
mwana?
Sangie
Sizikugwirizana,
Sangie
Mesa
tidzikondana
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Tell
me
why?
Ndiyankhe
Njuchi
akukakamire
Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.