Текст песни Mukanene (feat. BFB & Vinjeru) - Fredokiss
Mukanene
mukanene
Kaya
akutumani,
mukanene
Basi
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukanene)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukathoke)
Kaya
wakutumani,
mukanene
(Alaa)
Kaya
wakunamizani,
mukanene
(Shupiti)
Yemwe
wakutumani,
mukanene
Akupwetekesani,
mukanene
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukanene)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukathoke)
Nde
bwelelani
mukanene
(Eh)
Mwandikanika
kumene
(Eh)
Kubwela
mutabisa
nkhope
Kuyenda
ndi
midima
ngati
mileme
(Eh)
Munabwela
ndi
ti
njomba
ka
Mpaka
kutumiza
khobha
ka
Ghetto
simasunga
zoba
ka
Kanene
ntchana
ali
pompa
ka
Kundisemela
chi
nyau
(Nyau)
Kubwela
ndi
ti
mihau
(Hau)
Mwakumba
pasi
a
galu
Ngati
ma
bubu
mulibe
mawu
Mukanene
ku
MRA
You
can
tell
them
how
I
got
paid
Cause
I
be
hustling
all
day
Nali
ndende
but
I′m
okay
I'm
on
my
knees
mama
drop
cry
Conversating
with
the
most
high
Ghetto
glory
so
I
won′t
die
Fake
friends
wanna
know
why
Can
a
young
king
make
moves
anymore?
I
got
everybody
scared
trynna
blow
my
downfall
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukanene)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukathoke)
Kaya
wakutumani,
mukanene
(Mukanene)
Kaya
wakunamizani,
mukanene
(Mukathoke)
Yemwe
wakutumani,
mukanene
(Mukanene)
Akupwetekesani,
mukanene
Mukanene
mukanene
mukanene
(Pick
2)
Mukanene
mukanene
mukanene
Pitani
mukawauze
Zamabodza
zisandikhuze
Ntchana
Fredo
sangaluze
(Luze)
Only
weapon
is
the
most
high
(Most
high)
Mukanene
ku
police
(Police)
Fredokiss
ndiwa
peace
(Peace)
Young
boss
with
a
business
(Business)
Sindipanga
zau
tchisi
(Tchisi)
Mukanene
ku
chipani
(Pani)
Kodi
chimakhala
chani
(Chani)
Kumangopeka
zi
nkhani
(Nkhani)
Kapena
mwatha
ma
plan
(Plan)
Makape
busy
pa
Fb
(Fb)
Two
eyes
but
they
can't
see
(Can't
see)
Angokupweteketsani
(Tsani)
Angokupepeletsani
(Tsani)
I′m
trynna
receive
all
my
blessings
(Yeh)
I′m
binding
your
spirit
of
envy
(Woo)
Now
I
see
why
you
hate
me
(Hate
me)
It's
all
because
God
blessed
me
(Bless
me)
Going
through
hell,
devil
knocking
on
my
door
Close
it
in
his
face,
I
will
never
sell
my
soul
Palibe
chinthu
anzanga,
chosatha
(Tauze
aise)
Palibe
chinthu
anzanga,
chosatha
(Palibe)
Nkhale
ufumu
umene,
umatha
(Umatha)
Nkhale
unyakwawa
umene,
umatha
(Most
def)
Nkhale
ubusa
umene,
umatha
(Ehe)
Nkhale
uPresident
umene,
umatha
(Basop)
Nkhale
moyo
umene,
umatha
Nkhale
chitsulo
chimene,
chimatha
(Lets
go)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukanene)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukathoke)
Kaya
wakutumani,
mukanene
(Mukanene)
Kaya
wakunamizani,
mukanene
(Mukanene)
Yemwe
wakutumani,
mukanene
(Mukanene)
Akupwetekesani,
mukanene
(Mukathoke)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukathoke)
Mukanene
mukanene
mukanene
(Mukanene)
Ghetto
makaveli
up
in
this
Chi
ntchana
aise,
Tizingochimangilila
kuchimangilila
ukuku,
chatuluka
aise
(Hahaha)
Malawi′s
most
wanted
(Hahaha)
Joseph
in
the
bible,
anamagidwa
Jesus
Christ
was
arrested
aise
Nelson
Mandela,
Martin
Luther,
Steve
Bicko
Orton
Chirwa,
Kamuzu
Banda,
Fredo
Mafana
ose
amene
ali
mkati
Mafana
ose
amene
ali
mkati
Kaya
ndi
Chichiri,
Maula,
Zomba
Mzuzu,
ku
ndende,
ku
rumphi
Aliyese
amene
akuchita
kuziwa
kuti
Aise
uli
mkati
komano
aise
sukuyenela
kukhala
mkati
Ghetto
Gutter
Africa
2020
Jah
guide
aise
Nthawi
yako
ikwana
aise
Ingoyesesa
kuti
aise
mabondo
ako
uziwa
user
aise
Jah
Jah
amamva
aise
Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.