Текст песни Kusasa Mawu - Gwamba
Ndiyimbila
yehovah
ine
.
Mpaka
kusasa
mawu
ine
wandipatsa
ka
girl
timaso
tamngero...
Ndiyimbila
yehovah
yoh
mpaka
kusasa
mawu
ine
Wandipatsa
ka
girl
timaso
tamngero
relo
ndisasa
mawu...
Yeah
ambuye
mwadyetsa
mbalame
zosalima.
Kundionetsa
njira
nditangoima.
Kufewetsa
moyo
wanga
ukulimba.
Mwandipatsa
mkazi
mkona
ndikuyimba.
Nditangomuona
thupi
langa
lose
kugwidwa
zazi.

Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.