Текст песни Ambuye Wanga - Naomi
Ambuye
wanga,
mbuye
wanga,
mbuye
wanga,
Ndagwa
pamapazi
yanu
ine
munthu
wamachimo
ine,
mbuye
wanga
2x
Wazizimuka
mtima
wanga
mbuye
mulungu
wachifundo
ine
mbuye
wanga
Ndazizwa
pama
chimo
yanga
simumanditailila
mbuye
wanga
ine
Muchifundo
chanu
Mbuye
mulungu
chifundo
chanu
ndichachikulu
ndavomera
ine
mwana
wanu
Ndikachimwa
simumandilanga
Mumandipasa
nthawi
yolapa
ine
machimo
yanga...
Lizzilitious.com
Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.