Phyzix - Pa Ntondo текст песни

Текст песни Pa Ntondo - Phyzix




Akumandikambirana
Pa ntondo akumakajedana
Ndimati ndikatengana ndi squad
Nde kuti pachema timayambira pa liquor
Kaya ndipa njale, wapansi, pa njinga
Lero timasuka bola osaponda minga
Ndimasowesa chisoni mwamasenga
Amanditcha Kondwani chifukwa ndimakondwa
Akakhala ma babie ndimadyetsa njomba
Amati ndine openga ofunika Zomba
Tipite Salima ku Kapumba
Pachi Malawi ku njoyer ndikudya mipunga
Yemwe akufuna kutitenga atitenga
Tipita kulikonse tifika or Nyanja



Авторы: Noel Chikoleka



Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.