Phyzix feat. Krazie G & BFB - Lay Low текст песни

Текст песни Lay Low - Phyzix feat. Krazie G & BFB



It's only entertainment, exclusive
(Hook)
Timangomenya ma beat, timadziwika Mzuzu B-Town and L-CITY Yeah
Timangomenya ma heat, tikakwela pa stage timasiya mbilri
Awo amatihater awo awo, koma imatifila chick yawo
Amatihater awo awo, hey I let go call me lay low
(Phyzix)
Ine ndi Gamba wa suit, I am from 25 and I rep L-CITY
Tinasintha ma levels, straight outta the ghetto uzandipeza pa office
Kufilika kwa ineyo sikwa season,
Chaka chilichose ndimatulusa ma ringtone
Competition ya ineyo ndi nsima timapikisana kupezeka nyumba zonse
Competition ina ndi instrumental, timapikisana kupezeka nyimbo zonse
Amanditcha Phyzo mfana wotha zinthuzi,
Ma baby akungonditenga zithunzi
Ma selfie ma selfie ndi selfie stick
Si ine short ngati Dizzo, ndine captain long John
Mfana womveledwa ngati mastern
Mfana wazigoli ngati Messi 10
(Hook)
(Kraizy G)
King katakwe eyy yoh eyy you (yes sir)
Odi... Mfumu katakwe ilipo? Ilipo iwe ukufunsa ngati ndaniso?
Kodi... Anthu akewa sagwilila ntchito?
Ntchito? Kwaiye ntchito ilibe ntchito... (huh)
Basi chete mfumu itiyankhule
Timafana todelelati nditibandule
Chaka Chino ma guy akupaka nditchule
Ndipo ma guys azingovina aise azingovina
Mfana ati Ali sick, akangomenya three bars bas
Akuti... Amupeza ndi ma asthma
Ndikuti ndikudwala zi marasmus
Looks ya hd mboni ndizimaplasmas
Ada... ndinafika nazo pauchitsiru
Moti mafana panopa, amangodibela skill
Uchitsiru aise... Ndili ndi skill
Ndinapha hip-hop, ndikupezekaso pa will
(Hook)
(Black falcon Bird -BFB)
Ife ndi nkhaza... We kill beats and the flows no limit
Mafana akunama, R.I.P to Mafunyeta no gimmick
It's just me and everybody supporting the movement
Heard'em you rappers we're going we're moving
Tell'em these we're winning no loosing
Remember I am smart, I am the one God has chosen
Kuwakupa mafana, mpakana akunena tchuzi
Sinanga ndine mfana wotenthetsa ngati juzi
Sinanga Iwo sioyimba, ine mtengo Iwo mthunzi
Kuphatikiza Ngwazi, Dr. Bingu ndi Muluzi
I've brought a new style called payele payele
Umayesa umatha, kagwele kagwele
And the verse that I have, dzamvele dzamvele
Mfana wadzimbidwa aka... haaa haaaa!!!
(Hook)
The End



Авторы: Bfb, Phyzix


Phyzix feat. Krazie G & BFB - Lay Low
Альбом Lay Low
дата релиза
12-09-2017



Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.