Phyzix feat. Sir Patricks - Golide текст песни

Текст песни Golide - Phyzix feat. Sir Patricks



Mmmh uuh mmmh
Yeah yeah yeah
Physix verse 1
Ndimadzuka ndikusekelera dairy
Unabweretsa chimwemwe
Moyo waine
Amafuna kundisokoneza ena
Koma chikondi changoti go! Go! Go!
Chili pa ine
Love yathu ndi yomwe yabeba pa line
Timachezera kuyankhulitsana pa line
Nkhani zathu sizimatha
Tikadula phone ma units atha
Ndikuna ndikubwezere zokoma
Moyo wanga umauvetsa kukoma (kukoma)
Ndiwe Golide wa Quality
Chikondi chako ndichochuluka mu quality
Uli ngat m'godi wanga neh
Okumba Golide waine
Ndizachite bwanj zi ntchito zosezi
Kukubwezera zokoma
(Every time!) Hunie hunie hunie
Umanditchula iwe
(Dady dady dady) anytime!
Umanditchula iwe



Авторы: Phyzix, Stich Fray, Tricky Beatz


Phyzix feat. Sir Patricks - Golide
Альбом Golide
дата релиза
12-09-2017

1 Golide



Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.