The Very Best - Hear Me текст песни

Текст песни Hear Me - The Very Best



CHICHEWA
Siyani dumbo
Siyani umbombo
Tatopa nazo kodi simukudziwa kuti lija ndi kale?
Siya umbanda
Siya zauchigawenga
Kodi watani iwe siukudziwa kuti kupha ndi sambi?
Siyani dumbo
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Siya kaduka
Siya zokonda kuba
Siyani chinyengo kuyambila lero tiyeni tikonze tsogolo
Siyani kugona
Siya kugona tulo
Kunja kwacha kodi simukuona kuti dzuwa latuluka?
Siya kaduka
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Hear me now
Dzaka makumi asanu
Zatha kufika lero
Mpaka lero umphawi
Ukungophabe dziko
Dzaka makumi asanu
Zatha kufika lero
Mpaka lero umphawi
Ukungophabe dziko



Авторы: Esau Mwamwaya, Johan Karlberg


The Very Best - Hear Me
Альбом Hear Me
дата релиза
17-11-2014




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.