Zeze Kingston feat. London SA - Njoka текст песни

Текст песни Njoka - Zeze Kingston feat. London SA

Talikila, talikila
Talikila, talikila
Ndati talikila, talikila
Talikila, talikila
Samakondwa zikamayenda, zikavuta kusekelela
Chilichonse ungapange basi busy kukhomelela
From Monday to Sunday, busy kusatila
Amakhala kuti, ndindani, amapanga chani eish
Samakondwa zikamayenda, zikavuta kusekelela
Chilichonse ungapange basi busy kukhomelela
From Monday to Sunday, busy kusatila
Amakhala kuti, ndindani, amapanga chani Eish
Munthu ndi njoka njoka
Osakomedwa naye, sekelela ndikudyele osakomedwa naye
Munthu ndi njoka njoka
Osakomedwa naye, tembenuka ndikulume osakomedwa naye
Munthu ndi njoka njoka
Osakomedwa naye, sekelela ndikudyele osakomedwa naye
Munthu ndi njoka njoka
Osakomedwa naye, tembenuka ndikulume osakomedwa naye
Munthu ndi njoka njoka
Munthu ndi njoka njoka
Munthu ndi, munthu ndi njoka
Munthu ndi, njoka!

Авторы: Robert Ching'amba

Zeze Kingston feat. London SA - In My Zone
Альбом In My Zone
дата релиза
09-12-2022

Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.