Armstrong - Ndamusowa Lyrics

Lyrics Ndamusowa - Armstrong



Kupita masiku angapo,
Osamuona kukhala ngati zaka
No texting, no hello saying darli
Sizikuenda
Usiku onse osagona
Masana kumaganiza iwe dona
Kalalaka mtakuona
Usiku onse osagona masana kumaganiza iwe donaa
Sindichitiraso mwina ine
Ndipita kwawo, kwawo konko
Mkamuuze ndimakukonda
Ndipita kwawo kwawo konko
Mkamuuze ndamusowa
Oh na na na ndamusowa
Oh na na na ndamusowa
Oh na na na ndimamukonda
Oh na na na ndimamukonda
Oh na na na ndamusowa
Oh na na na! ndamusowa
Mtima wanga umawa
Ukatalikira ndimadwala
Achina fever, ma injections
Can never heal me
Oh baiby, ndimasowa mtendere
Eeeh eeh hee
Usiku onse osagona
Masana kumaganiza iwe dona
Kalalaka mtakuona
Usiku onse osagona masana kumaganiza iwe donaa
Sindichitiraso mwina ine




Armstrong - Ndele
Album Ndele
date of release
01-11-2013




Attention! Feel free to leave feedback.