Lyrics Panado - Onesimus
Panado
panado
yeah
mmm
ma
headache
yeah
mmm
eeh
Panado
panado
mmm
eeh
Amakonda
miseche
Amakondwa
munthu
adzivutika
Zochitika
ngati
siopemphera
Daily
daily
busy
ntopola
Kubaya
ma
damage
Kuupasa
moyo
wanga
challenge
Machitidwe
awo
ngati
Judas
Makhalidwe
awo
ngati
njenjete
eeh
Amafuna
ndikokoloke
Amakhumbira
nditaphokoloka
Amafuna
ndisokoloke
Amafuna
mwina
nditakomoka
Amafuna
ndikokoloke
Amakhumbira
nditaphokoloka
Amafuna
ndisokoloke
Amafuna
mwina
nditakomoka
Ndi
nsanje
apatseni,
panado
panado
Panado
panado
Amweko
panado
panado
Panado
anado
Mutu
wakula
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka
mwina
ndi
nsanje
Kaduka,
mtima
wachigawega
Mutu
wakula
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka,
mtima
wachigawega
Samafuna
ndiyendere
njale
Samakondwa
ndikamadya
money
Zikandiyendera
amakoka
chibale
Zikamandivuta
andinyoza
kumbali
Koma
mulungu
andichita
balance,
I
relax
Amamenya
nkhondo
nditakhala
pansi
Adani
anga
onse
alemba
m'madzi
Samakondwa
nane
Amafuna
ndikokoloke
Amakhumbira
nditaphokoloka
Amafuna
ndisokoloke
Amafuna
mwina
nditakomoka
Amafuna
ndikokoloke
Amakhumbira
nditaphokoloka
Amafuna
ndisokoloke
Amafuna
mwina
nditakomoka
Ndi
nsanje
apatseni,
panado
panado
Panado
panado
Amweko
panado
panado
Panado
panado
Mutu
wakula
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka
mwina
ndi
nsanje
Kaduka,
mtima
wachigawega
Mutu
wakula
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka
ndi
nsanje
Kaduka,
mtima
wachigawega
Attention! Feel free to leave feedback.