Sage Poet - Compassion (feat. Tadala, Sagonjah & Game Plan) Lyrics

Lyrics Compassion (feat. Tadala, Sagonjah & Game Plan) - Sage Poet



Ndine munthu, Dziwa ndiwe munthu
Dziwa muli matsonono Kukoma
M'chikondi ndi anthu
Mwamavume chikondi kumanga
Osamakankhana tikhale mu chikondi, Chikondi
Ey yo Sage! Popanda Chikondi sindingakhale
Ndingokhala ngati mtengo oti siungabale
Ukakhala opanda mano siuswa phale
Chisankho ndimakonda wankulu ena burley
Ena amakonda kukonda ena kukondedwa
Idzamera ndi mbewu yapa nthaka or yopondedwa?
Nsambi kwa wa nsembe Nsambi kwa m'Levi
Dzuwa sungazembe Atelo ndi mlengi
Atelo alembi Ndikukonde ngati mwini
Ngakhale ukonda ngini Zopanda mwinimwini
Wadyela koma wa mabala mu usinini
Komabe mitima kutipula chikondi ndikufesa
Zoyipa kubzikula mwazi sindikukhesa
Kufunsa mafunso ngati sindikumvesa
Mesa zikakuchulula zimavuta kumeza
Ndine munthu, Dziwa ndiwe munthu
Dziwa muli matsonono Kukoma
M'chikondi ndi anthu
Mwamavume chikondi kumanga
Osamakankhana tikhale mu chikondi, Chikondi
The Omnipresent Love is above so below
Because Light is the electromagnetic in its form
Love is alive from the moment we are born
From the womb to the tomb these are lessons we should know
It keeps us warm, sometimes the Love is cold
Light creates and breaks the patience in the soul
It's in the heart, Light is what designs in mind
Love does not discriminate, Light has always been the kind
God Universal, Ruler Universal Law
So, no matter who you is, Light has balance of its own
It's unconditional receive with no judgement
It's compassion over others it's the universal coven
Light workers because Love nurtures us to the Oneness
So, the path of devotion to open to door to abundance
It's not far Love is not a distant star
Light is Anuk Ausar, God is Love that's who we are, Love
Ndine munthu, Dziwa ndiwe munthu
Dziwa muli matsonono Kukoma
M'chikondi ndi anthu
Mwamavume chikondi kumanga
Osamakankhana tikhale mu chikondi, Chikondi
Mulungu ndi chikondi,chikondi ndi Mulungu
Zinazi zipembezo anakonda munthu
Chikondi ndikukonda osasankhana mtundu
Chikondi ndikukonda osawonana khungu
Chikondi, lamulo la Mulungu limodzi
Mukonda bwanji Mulungu ngati simokonda umodzi
Zonama, chikondi sichikukamba zogawa
Zomanza, chikondi chikukamba zomanga
Chikondi, Wadala okondedwa wakonda
Kusiya kuwona chikondi ndichokongola
Chikondi chilibe chilendo sichimaphonya
Ngati unakhumudwa ndi chikondi chinali cha boza
Chikondi ndi cha ulele, ndi cha ulele
Sizongolandira nawenso upeleke
Chikondi ndi anthu ndi iwe ndi ine
Chikondi ndi anthu ndi ife
Ndine munthu, Dziwa ndiwe munthu
Dziwa muli matsonono Kukoma
M'chikondi ndi anthu
Mwamavume chikondi kumanga
Osamakankhana tikhale mu chikondi, Chikondi



Writer(s): Wongani Kawonga


Sage Poet - Parable of the Chariot
Album Parable of the Chariot
date of release
21-03-2021




Attention! Feel free to leave feedback.