Lyrics Mwazi - The Very Best
Ukakhala
iwe
mphwanga
Usadzinamize
uli
ndi
abale
Amakukonda
uli
ndi
chuma
Ukasauka
kukutaya
Amayiwala
kuti
mwazi
ndi
mwazi
Umawundana
kuposa
madzi
Iwe
iwe
mvera
Tchera
tchera
khutu
Ganiza
ngati
munthu
1 Yalira
2 Chalo
3 Whoa
4 Mwazi
5 Nsokoto
6 Angonde
7 Julia
8 Mfumu
9 Ntende Uli
10 Rain Dance
11 Kamphopo
12 Kada Manja
13 Zam'dziko
Attention! Feel free to leave feedback.