Lyrics Njoka - Zeze Kingston feat. London SA
Talikila,
talikila
Talikila,
talikila
Ndati
talikila,
talikila
Talikila,
talikila
Samakondwa
zikamayenda,
zikavuta
kusekelela
Chilichonse
ungapange
basi
busy
kukhomelela
From
Monday
to
Sunday,
busy
kusatila
Amakhala
kuti,
ndindani,
amapanga
chani
eish
Samakondwa
zikamayenda,
zikavuta
kusekelela
Chilichonse
ungapange
basi
busy
kukhomelela
From
Monday
to
Sunday,
busy
kusatila
Amakhala
kuti,
ndindani,
amapanga
chani
Eish
Munthu
ndi
njoka
njoka
Osakomedwa
naye,
sekelela
ndikudyele
osakomedwa
naye
Munthu
ndi
njoka
njoka
Osakomedwa
naye,
tembenuka
ndikulume
osakomedwa
naye
Munthu
ndi
njoka
njoka
Osakomedwa
naye,
sekelela
ndikudyele
osakomedwa
naye
Munthu
ndi
njoka
njoka
Osakomedwa
naye,
tembenuka
ndikulume
osakomedwa
naye
Munthu
ndi
njoka
njoka
Munthu
ndi
njoka
njoka
Munthu
ndi,
munthu
ndi
njoka
Munthu
ndi,
njoka!
Attention! Feel free to leave feedback.