Zeze Kingston feat. Temwah & Jillz - Mvetsela Lyrics

Lyrics Mvetsela - Jillz , Zeze Kingston




Ndabalalika, ndabalalika
Oh! ndabalalika ndabalalika
Ndabalalika, ndabalalika ndabalalika
Mafuta akwela
Sopo wakwela
Ndiwo zakwela
Eish, zavuta
Mafuta akwela
Sugar wakwela
Rent yakwelanso
Ayi zavuta
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndalama zanga ndipatse ndipatse
Ndabalalika, ndabalalika
Oh! ndabalalika ndabalalika
Ndabalalika, ndabalalika ndabalalika
Mafuta akwela eish
Mafuta akwela
Rent yakwelanso ah ah ah
Mafuta akwela
Rent yakwelanso ah ah ah
Nndipatse ndipatse
Ndipatse ndipatse
Wangongole yanga ndipatse ndipatse
Ndipatse ndipatse



Writer(s): Robert Ching'amba


Zeze Kingston feat. Temwah & Jillz - In My Zone
Album In My Zone
date of release
09-12-2022



Attention! Feel free to leave feedback.