Eli Njuchi - Phone paroles de chanson

paroles de chanson Phone - Eli Njuchi



Njuchi
Oooh yeah
These were the words he said
Tilimu depot
Ndisana nyamuke
Ukadusa Dedza
Dzayimbe phone
Lemme know if you gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Ayi mwanawe bus ndi iyo kazipita
Koma kwela usayang'ane mbuyo
Zikakayenda kwinako
Don't you ever forget where you are coming from
Dzayimbe phone
Lemme know if you gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Ukakafika dzandiyimbile
Map ndizaku londelele
Ukakafika dzandiyimbile
Incase unga dzaponde ndele
Nthawi yomweyi
Makula nsanga
Ooh I'm gonna miss you Chifu
Mwana wanga
Moyo ngosavuta
Kwa okhawo oziwa Chauta
Dzikakafika povuta mvera n'kuuze chokachita
Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you are lonely
Dzayimbe phone
Tizakhale pansi tiza kochane
Ndati dzayimbe phone
Lemme know if you gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Mukunkako chonde kumakalimbika
Kumakalimba zinthu zikamakafoka
Osasintha mtima womazichepesa
Tizibwana tingapo kumazilesa
Zikakavuta zatiyimbile
Za whatsapp Ife ndi kumadzele
Amuna samazipasa malile
Sizoti kungo kwiya basi mupakile
Tili kuno tikudikila
Ndipo kwathu ndikuyamikila
A Eli Njuchi ndithudi mwakula
Nambala ndi iyo zikamakakula
Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you are lonely
Dzayimbe phone
Tizakhale pansi tiza kochane
Dzayimbe phone
Lemme know if you gonna be okay
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Dzayimbe phoneee iiih oh yeah eeh
Dzayimbe phoneee iiih oh yeah eeh
Dzayimbe phoneee niii oh yeah eeh
Dzayimbe phone
Dzayimbe phone
Ndikafika pothodwa ndithu ndi mayimba phone
And then he tells me son osagonja
Usawapase chokamba ana
Usakondwelese mdani
Ukamagona yimba phone
Kwa Namalenga ndizotheka
Yimba phone
Yimba phone
Dzayimbe phone
Anytime when you feel like you are lonely
Dzayimbe phone
Tizakhale pansi tiza kochane
Ndati dzayimbe Phone
Lemme know if you gonna be okay
Dzayimbe phone
N'dzayimbe phone
Oh yeah
Dzikazavuta ndati n'dzayimbe phone
Ndati dzikazavuta ndithu n'dzayimbe phone
Zikazavuta ndati n'dzayimbe phone
Ndati dzikazavuta ndithu n'dzayimbe phone
Dzikazavuta mwana udzayimbe phone
Ndati dzikazavuta mwana udzayimbe phone
Dzikazavuta mwana udzayimbe phone
Ndati dzikazavuta mwana udzayimbe phone



Writer(s): Eli Njuchi


Eli Njuchi - The Book of Eli
Album The Book of Eli
date de sortie
16-12-2020




Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.