paroles de chanson Ziloleni - Eli Njuchi
Mamawa
dzuwa
kuli
mame
You
see
me
passing
by
everyday
M'manja
muli
saka
I
know
you
follow
me
Muma
ndi
londola
mobisa
Pomwe
ndadusa
pamakhala
mbeu
Mukandifunsa
sin'bisa
Ndine
mlimi
Kwanga
nkufesa
Mbeu
yangayi
njowala
Ngati
nyenyezi
Ndikawawuza
nde
samandimvesa
Chita
manyazi
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ndati
lolani
ziphukile
ngati
mtengo
Ngati
nthambi
zibale
zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Lolani
ziphukile
ngati
mtengo
Ngati
nthambi
zibale
zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ok
sispensa
Tiye
tiyambilenso
Mamawa
mpaka
kumadzulo
Ntchito
Yako
malipiro
Siwu
zina
zimapondedwa
Zina
kudyedwa
ndi
mbalame
Zochepa
zingapo
zimasamalidwa
Zimandikhudza
nsaname
Mbeu
zipase
musaziyang'anire
Ndiza
ntsogolo
zizandisamalire
Ndipo
musadabwe
nkati
ndi
thilire
Zimela
zagwerapo
olo
mundisesele
Olo
musazitipulire
Muzazi
wona
zikukula
Olo
musazitipulire
Muzazi
wona
muzazi
wona
zikukula
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphikile
Ndati
lolani
ziphukile
ngati
mtengo
Ngati
nthambi
zibale
zipatso
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
Ziloleni
Ziphukile
(ooh)
Lolani
ziphukile
ngati
mtengo
Ngati
nthambi
zibale
zipaso
Ziloleni
Ziphukile
Zili
ngati
mwini
nyimbo
Lolani
ndifese
mbeu
yaluso
Musandiweluze
kamba
ka
nsinkhu
(Ooh
yeah)
Abale
fesani
mbeu
Ziphukile
Musazibise
fesani
Ziphukile
1 Phone
2 Ma Ine
3 Ziloleni
4 Confess
5 Ghetto Survivor
6 One & Only
7 Honest
8 I Know
9 Marry You
10 As You Are
11 Nyimbo
12 Ululu
13 Naomi
14 Maria (feat. Faith Mussa)
15 Look Around
16 Sindizasiya
17 Kumpanje
18 Count Your Blessings
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.