The Very Best - Mwazi - traduction des paroles en anglais

Paroles et traduction The Very Best - Mwazi




Mwazi
Mwazi
Ukakhala iwe mphwanga
If you become rich
Usadzinamize uli ndi abale
You should not forget the one who stood by you when you were poor
Amakukonda uli ndi chuma
Those who only love you because of your wealth
Ukasauka kukutaya
Will leave you when you lose it
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
They will forget that blood is thicker than water
Umawundana kuposa madzi
And that thicker than blood there is nothing
Iwe iwe mvera
You, listen
Tchera tchera khutu
Listen attentively
Ganiza ngati munthu
Think like a human being





Writer(s): Esau Mwamwaya, Johan Karlberg, Etienne Tron De Bouchony De Berard De


Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.