paroles de chanson Nsokoto - The Very Best
Kumsokoto
kuli
mfiti
imodzi
inkalodza
ana
osalakwa
Kupata
kwa
ana
iyo
sinkasangalatsidwa
nako
Mwana
apate
eti
tiona
ngati
agone
Chaka
chino
chokha
iye
akagonera
kumanda
M'mati
n'kwere
ndakwera
panyumba
yanthakati
Wakoma
bana
pawaka
Wamara
bana
nsokoto
Mwana
akangoti
agone
Kum'bwerera
usiku
Thupi
lonse
lamangika
Kulephera
kufuula
Poti
adsuke
mam'mawa
Thupi
kunjenjemera
Mutu
wanga,
malungo,
matenda
aja
akula
Wakoma
bana
Wati
kitasha
Wamara
bana
Ichi
n'chasoni
Nsokoto
nsokoto
Nsokoto
nsokoto
Muuze
nthakatiyo
namulondola
ife
takana
Bana
bakunsokoto
ise
Bana
bakumulowe
ise
Bana
bamwakisulu
ise
Bana
bakaronga
ise
Bana
bakurumphi
ise
Bana
bakuchitipa
ise
1 Yalira
2 Chalo
3 Whoa
4 Mwazi
5 Nsokoto
6 Angonde
7 Julia
8 Mfumu
9 Ntende Uli
10 Rain Dance
11 Kamphopo
12 Kada Manja
13 Zam'dziko
Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.