The Very Best - Mwazi paroles de chanson

paroles de chanson Mwazi - The Very Best




Ukakhala iwe mphwanga
Usadzinamize uli ndi abale
Amakukonda uli ndi chuma
Ukasauka kukutaya
Amayiwala kuti mwazi ndi mwazi
Umawundana kuposa madzi
Iwe iwe mvera
Tchera tchera khutu
Ganiza ngati munthu



Writer(s): Esau Mwamwaya, Johan Karlberg, Etienne Tron De Bouchony De Berard De



Attention! N'hésitez pas à laisser des commentaires.
//}