Roberto - Mtima Wako текст песни

Текст песни Mtima Wako - Roberto




Siniziba po yambila koma nizayesa kufotokoza
Chibe chinjenje mesa, ninshi namu mimba mwayambo bila
Nikuziba koma suniziba, chipaya nimanja na nsoni zanga
Kuwama kwako mwandi ivi veuchita vikulinga
Nima kumbwila nthawi zonse camera iyi ni witness
Navitunzi veutenga mwaendo patika mu magazine
Vina mu newspaper, vina pa internet
Chalo chonse chikuziba but nifela
M'tima wako, baby
Wako (m'tima)
M'tima wako. baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako
Mwezi uyu ukayaka nigona nishi nikulota
Daily kungo pindamuka mutu ine nao unipwanya
Maso ve awona singa linganise ku muntu wina
Nalema kuku kumbwa, lelo chibe bwanji tizazibana
Nivomo kupelekeza konse kweufuna
Ni nthawi yenifuna nokuti ise tichezeko
Siniziba we ufuna, manager or accoutant
Mu coloured or musungu ndaba nifela
M'tima wako, baby
Wako (m'tima)
M'tima wako, baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako
Nivomo kupelekeza konse kweufuna
Ni nthawi yenifuna, ndaba nifela
M'tima wako, baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako
M'tima wako, baby
Wako




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.