Suffix - Kwanu Nkwanu - перевод текста песни на английский

Текст и перевод песни Suffix - Kwanu Nkwanu

Kwanu Nkwanu
Kwanu Nkwanu
Listen
Listen
Bambo anga ankandikhazika
My father is writing to you
Pansi ndili mwana wovuta
Because you are a difficult child
Ndili chakusekondale here ndisakuganizaso zoyimba
Do you think I am just playing around? I am not thinking of singing
Mwana wanga ndithu kukula
My child, you really are growing up
Ife taonapo yambili mvula,
We have seen many rains,
Ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu kumanda.
You are the first born, we are depending on you, you will grow up and go to the grave quickly.
Kusukulu komwe uliko, uzikumbuka komwe uchokela,
At the school you are at, you will remember where you are from,
Nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe analowela.
I also did not know where I went, I had a lot of struggles.
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Know, know, know, my child, know, know, know, my child, know
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Know, know, my child, know, know, my child, your home, your home, your home
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
My child, your home, your home, your home, my child, your home, your home
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh
Your home, my child, your home, your home, your home, my child, eeehhh
Ya, life sikhala fair, macritisism sabweletsa sheda,
Yeah, life is not fair, criticism brings no peace,
Aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela,
Everyone has their preferences, if they don't like your preferences, don't take it to heart,
Kumasiyanitsa azako ndiabale, ena utavutika sangathandize m'bale,
It is important to differentiate friends from family, some will not help you when you are in need,
Osamatengeka akamakuchemelera enawo
Don't be fooled when they call you, others
Ukazazizila azakupanga chandamaleee
You will be disappointed, they will make you sad
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Know, know, know, my child, know, know, know, my child, know
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Know, know, my child, know, know, my child, your home, your home, your home
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
My child, your home, your home, your home, my child, your home, your home
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh
Your home, my child, your home, your home, your home, my child, eeehhh
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Know, know, know, my child, know, know, know, my child, know
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Know, know, my child, know, know, my child, your home, your home, your home
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
My child, your home, your home, your home, my child, your home, your home
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh
Your home, my child, your home, your home, your home, my child, eeehhh

Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.