Suffix feat. Pompi - Kutali текст песни

Текст песни Kutali - Pompi , Suffix



Yeah, Tribulations are pluses
Better learning,
Get access to your deepest desire
God is still on the mountain yeah yeah
Wazizur
Tinayambira Chilobwe ghetto
Ku Naotcha mpira pachimtengo
Kuba ma khodo kukalowa video show
Ayimike dzanja amene sanachimweko
Madala ankandiphika heavy
Anasiya ndili Form 3 musandiseke
RIP to my friend Mwale Isaac
Bwenzi pano tikuseka za umwana waife
Ifeso tavinako Kwaito
Ma battle ku Trade Fair umadziwa zapadziko
Fast forward Chiradzulu Seco-ndary
Kubwereza Form nkukumana ndi Jackson
Ndinayamba kuimba chifukwa cha iwe
Armstrong fresh kutsegula Studio yaife
G-Dox TK tapangakoso ma (instru)mental
Kenako anditrapa CU kukapanga Ecoz
Freshmen Likey Mopreme and Ivan
Then I got saved
Holy Culture achina Chapters
Radio 2 played DOS for the first time
Tinali trip ya SCOM ku nyanja tinapenga
Don't you worry
The vision might tarry
Pali nkhani ya Destiny sungaisakire patali
Patience, its a journey ndi safari
Kwe tichoka ndi kutali
Patience, it's a journey ndi safari
Kwe tichoka ndi kutali
I wanna be grateful not ungrateful yes
I wanna be thankful for your faithfulness
Munandilora andiweede pa CU
Kumaliza BIU ndinkayesa nzausilu
Kumazifunsa kodi Mbuye anandiweedilanji
Two months osathoka ndi madala pa den
Mavuto anga kukwezetsa BP yama sten
I had to break from music kuti ndimalize geri
Mentor Truth, Sho Baraka 'cause of music
Did a song with Pompi Sho Baraka what a blessing
As about me I'm fine with my music
Got a job with YoungLife Malawi what a blessing
My last KBG achina Liwu, New Don, dad, all my fans God bless you
Joy, Sley, GD, GD, Blage, Faith Mussa, all things work for the good
Munandiphusha
See everybody has a story
See everybody has calling
Ambuye mwandichotsa kutali
Ndikuyamikani Ambuye ndinu patali
See everybody has a story
See everybody has calling
Ambuye mwandichotsa kutali
Ndikuyamikani Ambuye ndinu patali
Don't you worry
The vision might tarry
Pali nkhani ya Destiny sungaisakire patali
Patience, its a journey ndi safari
Kwe tichoka ndi kutali
Patience, it's a journey ndi safari
Kwe tichoka ndi kutali




Suffix feat. Pompi - Before I Sleep
Альбом Before I Sleep
дата релиза
11-05-2018



Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.