Suffix - Kwanu Nkwanu текст песни

Текст песни Kwanu Nkwanu - Suffix

Listen
Bambo anga ankandikhazika
Pansi ndili mwana wovuta
Ndili chakusekondale here ndisakuganizaso zoyimba
Mwana wanga ndithu kukula
Ife taonapo yambili mvula,
Ndiwe first born ife tikudalila, ukafuntha uzapita mwachangu kumanda.
Kusukulu komwe uliko, uzikumbuka komwe uchokela,
Nanenso nnali ndiazizanga ambili sindziwa komwe analowela.
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh
Ya, life sikhala fair, macritisism sabweletsa sheda,
Aliyense ali nzokonda zake, akadana ndizokonda zako usamawatengela,
Kumasiyanitsa azako ndiabale, ena utavutika sangathandize m'bale,
Osamatengeka akamakuchemelera enawo
Ukazazizila azakupanga chandamaleee
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh
Dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa dziwa mwana wanga dziwa
Dziwa dziwa mwana wanga dziwa dziwa mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu
Mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu
Nkwanu mwana wanga kwanu nkwanu nkwanu mwana wanga eeehhh

Suffix - Before I Sleep
Альбом Before I Sleep
дата релиза
11-05-2018

Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.