Gwamba - Sindichoka (feat. Beracah) текст песни

Текст песни Sindichoka (feat. Beracah) - Gwamba



Zambiri yanu ndinamva akhungu onse osamva enawo sayenda kungowakhuza
Inu nyengo zawo zinasitha nane ndifuna mundikhudze chonde
Musandipitilire ndatsegula manja mulore zimu wanu mwa ine ukhazikike
Yesu anamva mphamvu zikuchoka zimai wina wina wake atugwira mavuto
Ake onse ndikuchoka amadwala bas iye ndi kuchira nane mbuye wanga
Mundigunde mukandiolose pa mafunde ndikudziwa pena
Ndine khutukumve koma mukafuna kukandi user mundi user
Mukandikhudza nyengo zanga zisitha mukandikhuza nyengo zanga
Mumachita zazikulu izo ndinamva simkaika konse I wanna see your glory
I wanna testify ukulu wanu ndiuone kma sindichokachokachoka mpaka
Mundikhudzekhudzekhudze kma
Sindichokachokachoka mpaka mundikhudze ine
Mbuye wanga chonde mundikhudze ndikalakwisa chonde mundiuze
Ndikamachepa chonde mundikuuze osalora satana andi zunze zolakwika
Zonse muzichotse inu ndamene mungakonze pandekhapa palibe
Chomwe ndingachite nde chonde muzindisamalira nthawi zonse
Chonde musalore moyo wanga satana adzaleponso adzalemo zoti
Sizanga chonde musalore mbuye wanga satana akolope moyo mwanga
Mukandikhudza nyengo zanga zisitha mukandikhudza nyengo zanga
Mumachita zazikulu izo ndinamva simkaika konse
I wanna see your glory I wanna testify ukulu wanu ndiuone kma
Sindichokachokachoka mpaka mundikhudzekhudzekhudze
Kma sindichokachokachoka mpaka mundikhudze khudze ine
Mpaka mundikhuze ine
END




Gwamba - Mama Said God First
Альбом Mama Said God First
дата релиза
29-09-2019




Внимание! Не стесняйтесь оставлять отзывы.