Lyrics Mtima Pansi (feat. Onesimus) - Gwamba
Uyike
ntima
pansi
Usadandaule
khala
pansi
Zonse
ndi
nthawi
basi
Usamasweke
ntima
n'zinthu
zazing'ono
Gwada
Yehova
akugwile
nkono
Tadekha
Tadekha
Yeeeeiiieeeeh
Aaaa
aaaa
aaaa
aaaaah
Oooo
oooo
ooooh
ooh
oh
Uh!!
Gwada
kwa
Ambuye
ndi
mavuto
ako
Akafuna
kuyankha
samafunsa
nzako
Muuze
zonse
zokhumba
za
ntima
wako
Ndi
wamkulu
heavy
kuposa
vuto
lako
Eish!
Ndiyekhayo
yemwe
angakukonze
Anawolotsa
nyanja
achina
Mose
Akhale
patsogolo
zinthu
zonse
Olo
utachimwa
buanj
akudzodze
Osadanda
mphanga
izi
nzazing'ono
Yehova
wakumwamba
ali
ndi
chisomo
Ika
manja
m'mwamba
akugwile
nkono
Uyike
ntima
pansi
Usadandaule
khala
pansi
Zonse
ndi
nthawi
basi
Usamasweke
ntima
n'zinthu
zazing'ono
Gwada
Yehova
akugwile
nkono
Tadekha
Tadekha
Aaaahh
aaaah
aaah
aaahh
Oooo
ooooh
ooooh
oooh
Uh!
mwetulira
mphwanga
usanyasitse
nkhope
Akachedwa
kuyankha
usatope
Umawelenga
Bible?
Ana
a
Mulungu
anayenda
pansi
Kwa
zaka
40
Mlaliki
paguwa
kulalikira
agonthi
Maso
patsogolo
iwe
si
Mkazi
wa
Loti
Panyanja
yamachimo
pati
floater
Ngati
boat
Machimo
mu
ntima
mwako
kupanga
deport
Eish!
Mphepo
yaukali
Yahwe
akugwila
nkono
ufika
kutali
Ndati,
mphepo
yaukali
Akayendetsa
Yahwe
moyo
wako
N'wawutali
Uyike
ntima
pansi
Usadandaule
khala
pansi
Zonse
ndi
nthawi
basi
Usamasweke
ntima
n'zinthu
zazing'ono
Gwada
Yehova
akugwile
nkono
Tadekha
Tadekha
Yeeeiiiyeeee
Aaaah
aaah
aaaah
aaaaaaah
Ooooh
oooh
ohhhhh!
1 Oba (feat. Nimix & Tay Grin)
2 You Are Everything (feat. Tumi)
3 Mtima Pansi (feat. Onesimus)
4 Final Say (feat. Dan Lu)
5 Akondakitale (feat. Lawi)
6 Sindichoka (feat. Beracah)
7 48 Bars for Christ
8 Unatha
9 That's a No No (feat. Jillz)
10 Higher (feat. Nimix)
11 Give Me Love (feat. Praise Peterson)
Attention! Feel free to leave feedback.