Lyrics Unatha - Gwamba
Intro
(Gwamba)
Ase
Gwamba(mmmh)
uli
kutiko?
(Ndikuvaya
ku
church
aise)
Iyayi,
panopa
tacaller
Zima
chick
aise,
Kuli
zi
ma
chick
6 zinazake
(Iyayi
man
Ndikuvaya
ku
church
ase)
4 za
ku
CU,
2 za
ku
DMI
(Iii
ase
Lero
nde
Friday
nde
timavaya
ku
church)
Tagula
mikunda,
shisha,
inunso
amwene
(Simungazimvetse)
Yo
Unali
kale
aise
uli
ndi
ma
chick
ten
Amachita
kukumana
kupasana
ma
turn
Lero
kubwela
Mary
mawa
kubwela
Jane
Pakamwa
pako
Nthawi
zonse
Mary
Jane
Pano
kukucaller
Friday
uli
ku
church
Team
yamadolo
mphwanga
uli
pa
bench
Iwe
kumapemphela
ife
tikuwupeza
Man
Gwamba
anakupusitsani
Major
Timamenya
drug,
Timamenya
bagi
Maluzi
kubwela
iwe
kupinyulitsa
Shati
Nthawi
Zina
akabwela
kupinyulitsa
car
key
Umakonda
mabomba
timakutcha
Iraq
UNALI
KALE
IWEEE
Pano
suzitsata,
tikamenya
beef
nanga
bwanji
sutiyankha
UNALI
KALE
IWEEE
Pano
suli
ghatta,
ukuimba
zotukwana
muja
unkatiwaza
×2
Nde
Man
Gwamba
simubwela?
EHHHHH
AISEE
DAMAN
(Shut
up
in
Hebrew)
Zomwe
mupangazo
ndinapanga
kukuposani
Ndikudziwa
bwino
moyo
musapange
makani
Kuzitchela
nokha
mawali
muli
pampani
Man,
zimenezo
mumapindula
chani?
Kuononga
dola,
kufuna
kuballer,
Mawa
kufuna
kugula
phax
nthumba
osalola
Mwadzuka
ndi
Flora,
komano
ndi
mbola
Chifukwa
aliyense
Ali
ndi
dola
amamucaller
Komani
man,
ndinu
friend
osamakhala
chonchi
Mumuyese
Yesu
Khristu
otifela
pa
cross
Mukapeza
Nthawi
mutipezeko
ku
temple
Mawu
aNamalenga
aja
muzawamveko
UKALE
KALE
IWE
UNALI
KALE
IWE
GWAMBA
UNALI
KALE
IWE
UNATHA
(AK)
Ayayayayayaya
Ayeeeeye
Ayayayayayaya
Ayeye
Ayayayayayaya
Ayeye
Ayayayayayaya
Ayeye
You
can
download
the
song
below
Attention! Feel free to leave feedback.